Sitigawana

Rudimental & Faith Mussa - Pop
Sitigawana
0 Plays
Duration: 4:17
Lyrics
[Verse] A Phiri anabwela kuchoka ku Harare eeh A Phiri anabwela kuchoka ku Harare eeh Koma nkati mwa suitcase Munalibe kanthu shuwa Ndati nkati mwa suitcase Munalibe kanthu shuwa A Phiri anaganiza kodi ndidzayenda kuti? Makolo anga onse anamwalira ku Dara A Phiri anaganiza kodi ndidzayenda kuti? Makolo anga onse anamwalira ku Dara [Pre-Chorus] Koma nkati mwa suitcase Munalibe kanthu shuwa Ndati nkati mwa suitcase Munalibe kanthu shuwa A Phiri anaganiza kodi ndidzayenda kuti? Makolo anga onse Anamwalira ku Dara Anamwalira ku Dara Oh, sitigawana [Chorus] Oh, sitigawana Sitigawana Oh, sitigawana zida Umandikondera M'mene umandikondera Ife Sitigawana zida Sitigawana Sitigawana zida Sitigawana Ife sitigawana, sitigawana Oh, sitigawana zida Sitigawana Sitigawana Oh, sitigawana zida Umandikondera M'mene umandikondera Ife sitigawana zida Sitigawana Sitigawana Oh, sitigawana zida Umandikondera M'mene umandikondera Anamwalira ku Dara [Outro] Koma nkati mwa suitcase Munalibe kanthu shuwa Ndati nkati mwa suitcase Munalibe kanthu shuwa A Phiri anaganiza kodi ndidzayenda kuti? Makolo anga onse Anamwalira ku Dara A Phiri anaganiza kodi ndidzayenda kuti? Makolo anga onse Anamwalira ku Dara
Rate this song
0/5.0 - 0 Ratings
Loading comments...
Credits
- Writers
- Amir Amor
- Kesi Dryden
- Piers Aggett
- Leon “Locksmith” Rolle
- Christian Martinez
- Steve Martinez Jr.
- Nashil Kazembe
- Faith Mussa